M’modzi mwa akatswiri omwe amayankhulapo pa nkhani za mdziko muno, a Lyford Chadza, ayamikira boma kaamba kothetsa mlandu wa anthu atatu omwe adanjatidwa kamba kosokoneza galimoto zapa m’dipiti ponena kuti izi zidakaononga ubale wabwino pakati paboma ndi anthu aku Ndirande. Malingana ndi a Chadza, ati zomwe lachita boma ndichiyambi chokonza ndikumanga ubale wabwino pakati pa […]
The post Katswiri pa nkhani za ndale wati boma lachita chamuna pothetsa milandu ya anthu osokoneza m’dipiti appeared first on Malawi 24.