Katsonga ang’alula: Ati Malawi sikutukuka chifukwa timasankha atsogoleri opanda ndalama akamalowa m’boma

Nduna yakale yazamalonda a Mark Katsonga Phiri yati dziko lino likukanika kutukuka kamba koti anthu amavotera adindo omwe amalowa m’boma alibe ndalama komanso luntha lopanga ndalama koma kusakaza misonkho ya Malawi. Iwo alankhula izi pamwambo okhazikitsa mwala wamaziko pasukulu ya sekondale ya Ligowe pomwe pakhale malo ophunzilira komputa zomwe ati zithandizira kukweza maphunziro m’boma la […]

The post Katsonga ang’alula: Ati Malawi sikutukuka chifukwa timasankha atsogoleri opanda ndalama akamalowa m’boma appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください