Phungu wadera lakumvuma kwa boma la Rumphi a Kamlepo Kalua wati ndiwokonzeka kukhala nzika ya dziko la Tanzania ngati boma lipitilize kupereka ntchito za chitukuko mokondera. Polankhula mnyumba ya malamulo masanawa a Kalua ati mzodandaulitsa kuti boma likuyenera kukwanilitsa malonjezano ake pa nkhani ya chitukuko kudera lawo pofotokoza kuti kuli mavuto mavuto ambiri. Iwo ati […]
The post Kamlepo wakwiya, ati ngati boma lipitilize kukondera asamukira ku Tanzania appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.