Kalindo watuluka pa belo

Bwalo lamilandu munzinda wa Lilongwe latulutsa pa belo a Bon Kalindo pa milandu iwiri yopezeka ndi mfuti popanda chilolezo komaso kufalitsa nkhani za bodza pa masamba amchezo. A Kalindo omwe amadziwikaso ndi dzina loti ‘Winiko’, anamangidwa mchaka cha 2021 kamba kopezeka ndi mfuti popanda chilolezo komanso anamangidwa posachedwapa powaganiziridwa kuti anafalitsa uthenga wabodza pamasamba amchezo. […]

The post Kalindo watuluka pa belo appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください