Kalindo ampeza osalakwa

Omenyera ufulu Bon Kalindo, wayamba kuchotsera milandu yomwe akuzengedwa pomwe khothi ku Zomba lalamura kuti nkuluyu ndi mfulu pa mlandu oyambitsa zipolowe omwe amazengedwa m’bomalo.  A Kalindo omweso amatchuka ndi dzina lawo la pazisudzo la Winiko, anamangidwa m’bomali pa 23 November chaka chatha pomwe zionetsero zomwe anatsogolera m”boma la Zomba zinathera zipolowe.   M’mwezi wa January […]

The post Kalindo ampeza osalakwa appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください