Mtsogoleri wa Malawi First Bon Kalindo ali mu mzinda wa Zomba kuchita ziwonetsero zosakondwa ndi kugwa kwa mphamvu ya kwacha, kukwera kwa mitengo ya zinthu komanso kuchepa kwa malipiro anthu ogwira ntchito Boma. Ziwonetserozi zayambira pa bwalo laza masewero la Zomba Community Ground mpaka akapereke chikalata chamadandaulo ku office ya Bwana Mkubwa wa Boma la […]
The post Kalindo akuchititsa zionetsero ku Zomba appeared first on Malawi 24.