Joyce Banda ayamikila Chakwera kamba kolengeza kuti m’maboma 23 muli njala

Mtsogoleri wakale wadziko lino yemwenso ndi mtsogoleri wa Chipani cha Peoples Party (PP) Dr Joyce Banda, wayamikira mtsogoleri wadziko lino Dr Lazarus McCarthy Chakwera kamba kaganizo lake lolengeza kuti m’maboma 23 mwa maboma 28 ndi malo angozi zogwa mwa dzidzidzi maka kamba ka njala yomwe yakhudza madelaro. Poyankhula pa bwalo la zamasewera ku area 23 […]

The post Joyce Banda ayamikila Chakwera kamba kolengeza kuti m’maboma 23 muli njala appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください