Joshua Mbele waitanitsa zionetsero zoikira kumbuyo Martha Chizuma

M’modzi mwa anthu oyankhulapo pazinthu zosiyanasiyana makamaka pa masamba a mchezo a Joshua Chisa Mbele, ayitanitsa zionetsero sabata yamawa powonetsa kusakondwa ndi zomwe mkulu wa bungwe la Anti-Corruption Bureau, Martha Chizuma akukumana nazo. Kuitanitsidwa kwa zionetselozi kukutsatira zomwe wachita yemwe akuganizilidwa kuti wakhala akuchita katangale a Ashok Nair omwe akasumira a Chizuma pankhani ya zomwe […]

The post Joshua Mbele waitanitsa zionetsero zoikira kumbuyo Martha Chizuma appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください

コメントを残す

メールアドレスが公開されることはありません。 が付いている欄は必須項目です