Jetu walira chokweza pamene bungwe la Copyright Association of Malawi (COSOMA) silidamupatseko yachipuputa misonzi pamene bungweli lapereka makobidi kwa oyimba osiyanasiyana mdziko muno ndipo iye akufunsa kuti a COSOMA akumusala bwanji? Jetu wayankhula izi kudzera munkanema yemwe Malawi24 yaona ndipo izi ndi zomwe wafotokoza: “Eee ndikufunseni inu azibambo aku COSOMA ine ndi Jetu azanga onse […]
The post Inu azibambo a COSOMA mukundisala bwanji? Wafunsa Jetu appeared first on Malawi 24.