…watsindika zakufunika kwa ulamuliro wa mzigawo Mtsogoleri wa chipani cha Alliance For Democracy (AFORD) Enock Chihana wati chipani chawo sichilowaso m’gwirizano ndi zipani zina pa chisankho chikubwerachi ponena kuti akuona kuti nthawi yoti alowe m’boma yakwana. A Chihana anayankhula izi Lolemba pa msonkhano omwe chipanichi chinachititsa ku Ndirande mu mzinda wa Blantyre komweso chipanichi chimakondwelera […]
The post Ino ndi nthawi yathu, sitikhalaso m’nkhwapa mwa chipani china, watero Chihana appeared first on Malawi24.