Mudziwitseni Phungu Joseph Nkasa kuti analakwitsa. Mose wa lero ati sanali Mutharika, koma ndi a Timothy Mtambo. Atero eniake pomwe anapangitsa msonkhano wa atolankhani lero pofuna kukumbutsa kuti akadalipo. A Mtambo amene adachita chete pomwe boma la Tonse lidawapatsa unduna, ndipo samamvekabe ngakhale atachotsedwa, pa 27 April achititsa msonkhano wa atolankhani ku Lilongwe. Msonkhanowu omwe […]
The post Ine ndiye Mose ine – watero Timothy Mtambo appeared first on Malawi 24.