Timu ya Mighty Mukuru Wanderers yauza bungwe la Football Association of Malawi kuti liyimitse kaye masewero onse a mpikisano wa Airtel Top 8 pofuna kudikira chigamulo pa apilu yomwe ikufuna ipange ndipo yati apo bii, ikatenga chiletso ku khothi. Izi ndimalingana ndi chikalata chomwe tsamba lino lawona chomwe chalembedwa ndi kampani yoimilira anthu pa milandu […]
The post Imitsani kaye Airtel Top 8 yonse, apo bii tikatenga chiletso – yanyangala Wanderers appeared first on Malawi 24.