Madzi akupitilira kuchita katondo kumbali ya a Kondwani Nankhumwa omwe pano khothi lawakaniraso pempho lawo lomwe amafuna khothilo lisamve pempho la chipani cha Democratic Progressive Party (DPP) pa nkhani yofuna kuwachotsa pa udindo wa otsogolera zipani zotsutsa boma m’nyumba ya malamulo. Nkhaniyi ikudza pomwe m’mbuyomu a Nankhumwa omwe ndi phungu wa dera la pakati m’boma […]
The post Ikakuona litsiro siikata; khothi lakana Nankhumwa, atha kuchotsedwa pa udindo otsogolera zipani zotsutsa appeared first on Malawi 24.
Moni Malawi 
