ICTAM yatasa dzanja pa bungwe la  Immigration

Bungwe lowona za akatswili  pa  ukadaulo wa makina a ma kompyuta ndi  zipangizo za makono  la ICT- Association of Malawi (ICTAM) lati lili lokozeka kuthandiza  ndi ukadaulo udziwi wawo ku bungwe lowona za anthu otuluka ndi kulowa m’dziko muno la Immigration  pamene pakali pano  likukumana  ndi mavuto popanga ziphaso. Bungweli lati ilo monga bungwe lomwe […]

The post ICTAM yatasa dzanja pa bungwe la  Immigration appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください