Gulitsani zimenezi – a bwalo agangalama, ati nyumba ya Mphwiyo ipitebe pa msika basi

Ngati mumakhala mukufunafuna mwayi wa nyumba ku Area 43 anaimba Tay Grin kuja ndiye sunthirani pafupi. Ndi kutheka mayankho anu muwapeza pano. A bwalo ati nyumba ya a Paul Mphwiyo ilandidwe ndithu. Oweruza milandu wa ku bwalo lalikulu Mayi Ruth Chinangwa akana kuchitira chisoni mkazi wa Paul Mphwiyo amene amafuna kuti bwalo liyimitse kaye kuwalanda […]

The post Gulitsani zimenezi – a bwalo agangalama, ati nyumba ya Mphwiyo ipitebe pa msika basi appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください