Chipani cha Malawi Congress (MCP) chati ndichokhumudwa ndi zomwe chapanga chipani cha Democratic Progressive (DPP) pochotsa ma membala ake ena mu chipanicho kuphatikiza a Kondwani Nankhumwa; koma anthu ena akuti ukafuna kudziwa mbuyake wa galu, umatola duka ndikum’gweba nalo pomwe ena akuti agalu otumidwa aja adya zothira tameki ndipo mwini agaluwo wakwiya. Nkhaniyi yayamba pomwe […]
The post Genda galu kuti udziwe mwini wake: kuchotsedwa kwa anthu ku DPP kwakwiyitsa MCP appeared first on Malawi 24.