Galimoto za Porsche, Lamborghini zaonongeka ndi moto mu sitima yapamadzi

Wolemba: Gracious Zinazi Galimoto pafupifupi 4,000 za mtundu wa Porsche, Volkswagen, Lamborghini ndi zina zaonongeka ndi moto omwe wayaka mu sitima ina ya pamadzi pa nyanja yaikulu ya Atlantic. Sitimayi yomwe dzina lake ndi Felicity Ace, imachokera ku Emden mu dziko la Germany ndipo yayaka moto pafupi ndi zilumba za Azores mu dziko la Portugal. […]

The post Galimoto za Porsche, Lamborghini zaonongeka ndi moto mu sitima yapamadzi appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください

コメントを残す

メールアドレスが公開されることはありません。 が付いている欄は必須項目です