Ngakhale kuti mphunzitsi wamkulu wa timu ya miyendo ya dziko lino a Patrick Mabedi sanatulutse mndandanda wa osewera akunja omwe wawaitana pa mpikisano wa mayiko anayi, zadziwika kuti Gabadinho Mhango yemwe anathawidwa ndi ndege chaka chatha, waitanidwaso. Timu ya Moroka Swallows, ya ku South Africa, komwe Mhango ogoletsa zigoliyu amasewera ndi yomwe yatsimikiza za nkhaniyi […]
The post Gaba waitanidwaso ku Flames appeared first on Malawi 24.