Fostina Ndemba wapambana mpikisano wa Mzuzu Half Marathon

Fostina Ndemba ndi amene wathamanga kuposa atsikana anzake mu mpikisano wa Mzuzu City Half Marathon lero. Mtsikanayu analibutsa liwiro ngati kulibe mawa ndipo iye anathamanga mtunda okwana 21 kilomitazi pa ola limodzi ndi mphindi zokwana makumi awili ndi zisanu. Wachiwiri kupambana ndi Teleza Master ndipo iye anathamanga makilomita okwana 21 mu ola limodzi ndi mphindi […]

The post Fostina Ndemba wapambana mpikisano wa Mzuzu Half Marathon appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください