Timu ya mpira wa miyendo ya dziko lino Flames lero pa 26 March ikuyembekezereka kuthambitsana ndi Chipolopolo ya m’dziko la Zambia kulimbirana malo achitatu mu 4 Nations Tournament ndipo masewero ake ayamba 2 koloko masana. Lero lomwe lino, Zimbabwe ikomana ndi Kenya kulimbirana malo woyamba ndipo masewero ake ayamba 5 koloko madzulo. Zimbabwe inafika mu […]
The post Flames ithambitsana ndi Chipolopolo lero pa Bingu Stadium appeared first on Malawi 24.