Fizi ku KuHeS yafika pa K1 miliyoni

Sukulu ya ukachenjede ya Kamuzu University of Health Sciences yalengeza kukwera kwa sukulu fizi kuchoka pa K400,000 komanso K550,000 kufika pa K1 million pa chaka. Malingana ndi chikalata chomwe asayinira ndi a Chikondano Mussa yemwe ndi mlembi wamkulu ku unduna wazamaphunziro, kukweraku ndi kwa ophunzira omwe anayamba Maphunziro awo kuyambira chaka choyamba. Miyezi yapitayo masukulu […]

The post Fizi ku KuHeS yafika pa K1 miliyoni appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください