Fetereza sitigula ngati chitumbuwa – Chihana wauza boma la Tonse

…wati ngati atsogoleri sakudziwa kanthu za feteleza, afuse anzawo omwe akudziwa Mtsogoleri wa chipani cha Alliance For Democracy (AFORD) a Enock Chihana, wawuza akuluakulu a boma la Tonse kuti ngati sakudziwa zoyenera kuchita pa nkhani yogula fetereza, afuse zipani zina zomwe zili ndi ukadaulo ponena kuti fetereza samagulidwa ngati zitumbuwa. A Chihana amayankhula izi lachiwiri […]

The post Fetereza sitigula ngati chitumbuwa – Chihana wauza boma la Tonse appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください