FAM yakanira Wanderers kulepheretsa masewero ndi Silver Strikers mawa

Pomwe timu ya Mighty Mukuru Wanderers inatulutsa kalata lachiwiri yopempha FAM kuti ilepheretse masewero ake ndi timu ya Silver Strikers mawa pomwe yati ikufuna chilango chomwe yapatsidwa chiunikilidwenso, bungwe la FAM lakana pempholi ndipo lanenetsa kuti mawa ulipolipo wa nkhodzo za pusi pa bwalo la Kamuzu. M’mawa walero, lachiwiri timu ya Wanderers inatulutsa kalata yonena […]

The post FAM yakanira Wanderers kulepheretsa masewero ndi Silver Strikers mawa appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください