Engineer Vitumbiko Mumba walumira mano ndipo wanenetsa kuti iyeyo sanaluzepo zisankho choncho pa 8 August pano akayima ndikukatenga mpando wa wachiwiri kwa mtsogoleri wa chipani cha MCP. Iyeyu, poyankhula ndi kanema wa Times usiku wathawu, watemesa nkhwangwa pa mwala kuti palibe chikuwaopsa kuti chingawagwetse osatenga udindowu. “Chipani cha MCP chikufunika wachiwiri kwa mtsogoleri wachinyamata yemwe […]
The post Engineer Mumba walumira mano ndipo wanenetsa kuti: “Ndikuyima ndipo ndikapambana!” appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.