Maiko ambiri a chigawo cha kummwera kwa Africa akupempha thandizo kuchokera ku maiko ena kamba kokhudzidwa kwambiri ndi mphepo ya El Nino yomwe inayambitsa chilala maikowa ndipo zadzetsa kukolora zochepa. Izi zadziwika pamene tsogoleri wa dziko la Zimbabwe, Emmerson Mnangagwa walengeza kuti dziko lake lakhudzidwa ndi ngozi zogwa mwadzidzi kamba ka kupitilira kwa chilala chomwe […]
The post El Nino abweretsa njala mmaiko a kummwera kwa Africa appeared first on Malawi 24.