Dziko lino lili pa chiopsezo cholandiraso namondwe

Nthambi yowona za nyengo yati pali kuthekera koti namondwe yemwe akuyembekezeka kubadwa mnyanja ya m’chere ya India, akhoza kudzafika kapena kuyandikira kum’mwera kwa dziko lino. Malinga ndi nthambiyi, Namondweyu sanabadwe koma akuyembekezeka kubadwa mu Nyanja ya Mchere ya India pakati pa mayiko a Madagascar ndi Mozambique pofika Lamulungu lino pa 10 March, 2024. “Pali chiyembekezo […]

The post Dziko lino lili pa chiopsezo cholandiraso namondwe appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください