Dziko la Malawi silikugwiritsa ntchito  kwambiri  makondomu

Dziko la Malawi pamodzi ndi mayiko ena onse padziko lapansi lachiwiri pa 13 Febuluwale limakumbukira nawo tsiku la “Condom” pamene akatswiri ati a Malawi ambiri sakutha kupeza mwayi wa makondomu mwachangu. M’modzi mwa katswili owona za kulera ndi uchembele wabwino yemwenso ndi mkulu wa Family Planning and Association of Malawi (FPAM) Donald Makwakwa awuza wailesi […]

The post Dziko la Malawi silikugwiritsa ntchito  kwambiri  makondomu appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください