Chaka chilichonse pa 24 March ndi tsiku lomwe dziko la Malawi limakhala likukumbukira Matenda achifuwa chachikulu cha TB ndinso matenda a Khate, ndipo chaka chino mwambo okumbukira tsikuli ukachitikira m’boma la Mulanje. Malingana ndi mlembi Wankulu mu Unduna wa za Umoyo Dr Samson Mndolo, mutu wa chaka chino ndi wakuti ‘Zowonadi tikhoza kuthetsa TB, tigonjetse […]
The post Dziko la Malawi likhala likukumbukira Matenda a TB ndi Khate pa 24 March appeared first on Malawi 24.