…wati osamayankhulitsa chibwezi chikatha Akayanjana: patangodutsa sabata zochepa ochita zisudzo Tamia Ja atasambwadza bwenzi lake Duncan Nyoni kuti ndi owumira, pano awiriwa abwelerana ndipo mkaziyu wayamikira kuti mamunayu ndi wabwino kwambiri. Kuyambira sabata yatha pakhala pakuveka mphekesera kuti awiriwa omwe ubwezi wawo unatha mwezi watha, wabweleranaso; pajatu akuluakulu anati madzi samayiwala khwawa. Tamia Ja yemwe […]
The post Duncan ndi mamuna wabwino – watelo Tamia Ja appeared first on Malawi 24.