Wachiwiri kwa mtsogoleri wachipani cha DPP mchigawo chaku mmawa a Bright Msaka wati ndiokondwa kuti chipanichi chatenga mipando yonse ya m’makhonsolo mchigawochi. A Msaka ayankhula izi pambuyo pa chisankho cha wapampando wa khonsolo ya boma la Machinga. Khansala Simplex Diwa wasankhidwa kukhala wapampando ndipo wachiwiri wake ndi khansala Davis Weja. A Diwa ati […]
The post DPP yasosola mipando yambiri ya mankhasala ku Eastern Region appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.