Chipani cha Democratic Progressive (DPP) chati chili ndi chiyembekezo chodzatenganso boma pa chisankho chapatatu chomwe chikubwera chaka chamawa. Wachiwiri kwa mtsogoleri wa chipanichi m’chigawo chakum’mawa Bright Msaka wanena izi pa msonkhano wa ndale womwe unachitikira ku wadi ya Mwasa m’boma la Mangochi. Msaka adati boma lomwe lilipoli lalephera ndipo adanenetsa kuti DPP ndi chipani chokhacho […]
The post DPP yanenetsa kuti itenga boma chaka chamawachi appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.