DPP isakunamizeni, a Malawi akuvutika chifukwa cha katangale wawo, watero Moses Kunkuyu

Mneneri wa boma a Moses Kunkuyu wati mavuto azachuma omwe dziko lino likudutsa pano ndi kaamba ka katangale yemwe anali ochuluka kwambiri mu nthawi ya ulamuliro wa chipani cha Democratic Progressive (DPP). Poyankhula ndi imodzi mwa nyumba zofalitsa nkhani mdziko muno, Kunkuyu yemweso ndi nduna yazofalitsa nkhani, wati boma la MCP likukozaso ngodya zonse za […]

The post DPP isakunamizeni, a Malawi akuvutika chifukwa cha katangale wawo, watero Moses Kunkuyu appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください