DPP ikutinji lero? Atatu awonekera ku komiti yosungitsa mwambo

Lero komiti yosungitsa mwambo ku chipani chotsutsa boma cha Democratic Progressive (DPP) yakumana ndi a Kondwani Nankhumwa, Mark Botoman komaso a Cecilia Chazama koma osewa sakuulura momwe zathera, pamene a Grezelder Jeffrey sanafike kumaloku. Anayiwa anaitanidwa ku komiti yosungutsa mwamboyi kuti mwa zina akafotokoze bwino zifukwa zimene anaitanitsira komaso kuchititsa mkumano wa akuluakulu a chipani, […]

The post DPP ikutinji lero? Atatu awonekera ku komiti yosungitsa mwambo appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください