DPP ikufuna boma lilole kuti anthu opanda chiphatso cha unzika azavote nawo chaka cha mawa

Mtsogoleri wa aphungu achipani cha DPP mnyumba yamalamulo a Mary Navicha wati aphungu achipanichi apempha boma ndi bungwe la MEC kuti alole anthu ngakhale alibe chiphatso cha unzika koma anakwanitsa zaka zoponya voti kuti azawalore kuponya voti pachisankho cha chaka chammawa. A Navicha ati ganizoli ladza kutsatira kulephera kwa bungwe loona zakalembera wa unzika kulemba […]

The post DPP ikufuna boma lilole kuti anthu opanda chiphatso cha unzika azavote nawo chaka cha mawa appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください