Nthambi Yoona za Ngozi zogwa mwadzidzidzi (DoDMA) yomwe ili mu Ofesi ya Mtsogoleri wa Dziko Lino ndi Nduna, yati kuyambila m’mwezi wa October chaka chatha kufika mwezi uno, makhonsolo makumi awiri (20) m’dziko muno akhudzidwa ndi ngozi zogwa mwadzidzi. Izi zadziwika pamene nthambiyi imapeleka tsatanetsatane wa ngozi zogwa mwadzidzi ndi ntchito yopereka thandizo ku maanja […]
The post DoDMA yati makhonsolo 20 akhudzidwa ndi ngozi zogwa mwadzidzidzi chiyambileni nyengo ya mvula appeared first on Malawi 24.