Nthambi yoona za ngozi zogwa mwadzidzi m’dziko muno ya Department of Disasters Management Affairs (DoDMA) yati mabanja omwe ali ndikuthekera kogwira ntchito koma ndi a ulesi sazilandira thandizo la chimanga kuchokera ku Boma. Wanena izi ndi Mlembi Wamkulu ku nthambiyi, Charles Kalemba, m’mudzi mwa mfumu yaikulu Tengani m’boma la Nsanje, pomwe adapita kukakambirana ndi adindo […]
The post DoDMA yati mabanja a ulesi sazilandira chimanga chaulere kuchokela ku Boma appeared first on Malawi 24.