Nthambi yoona za ngozi zogwa mwadzidzidzi m’dziko muno ya DoDMa yalangiza maanja amene akulandila chakudya kuchokera ku boma kudzera ku nthambiyi kuti apitilize kugwira ntchito zawo za tsiku ndi tsiku kuti akhale odzidalira pawokha. Wanena izi ndi Mlembi Wamkulu ku Nthambiyi, a Charles Kalemba m’maboma a Karonga ndi Chitipa komwe amakhazikitsa ntchito yothandiza maanja omwe […]
The post DoDMA yalangiza maanja omwe akulandila chakudya kuti alimbikile ntchito zawo za tsiku ndi tsiku appeared first on Malawi 24.