DoDMA yakana kuti yagula nyemba ndi kapenta wa K200 miliyoni

Nthambi ya boma yowona za ngozi zogwa mwadzidzi ya DoDMA yakana mwantu wagalu malipoti oti yagwiritsa ntchito ndalama yokwana K200 miliyoni kugulira nsomba za kapenta komaso nyemba zopita kwa anthu omwe akhudzidwa ndi ngozi yakusefukira kwa madzi. Lachinayi mphekesera zinali ponseponse kuti nthambi ya DoDMA yagula nyemba komaso nsomba za mtundu wakapenta kuchokera mdziko la […]

The post DoDMA yakana kuti yagula nyemba ndi kapenta wa K200 miliyoni appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください

Generated by Feedzy