Disembala mafuta afika K900 — atero a Gwengwe

Pomwe anthu m’dziko muno analonjezedwa kuti vuto la kuthimathima kwa magetsi litha mwezi wa Disembala chaka chino, nduna yazachuma yati anthu ayembekezeso kuti mafuta agalimoto atsika mtengo kufika pa K900 mwezi omwewu. Nkhaniyi ikutsatira kutsitsidwa mtengo kwa mafuta a petulo omwe pano lita imodzi ikugulitsidwa pa K1746 kuchoka pa K1946 ndipo gasi ali pa K2600 […]

The post Disembala mafuta afika K900 — atero a Gwengwe appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください