Diamond Platnumz atutumutsa anthu pofika pa siteji ali m’bokosi

..mwini wake wati nayeso zinamuwopsa Gulu la anthu likupitilirabe kukambirana malodza omwe anapanga oyimba otchuka m’dziko la Tanzania Diamond Platnumz yemwe anafika pa malo oyimbira ali m’bokosi lomwe linanyamulidwa ndi anthu ovala zovala za makaka akuda. Lamulungu lapitali pa 10 September, kunali phwando la mayimbidwe lotchedwa ‘Wasafi Festivals 2023’ ku Ruangwa m’dziko la Tanzania komwe […]

The post Diamond Platnumz atutumutsa anthu pofika pa siteji ali m’bokosi appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください