Dedza Dynamos yatola chi 100 million 

Kunali kumwemwetera chakumasanaku ku Dedza pamene timu ya Dedza Dynamos yatembenuza chikwangwani nkukhala Premier Bet Dynamos kutsatira mgwilizano omwe timuyi yasayinira ndi kampani ya Premier Bet wandalama zokwana 100 miliyoni kwacha. Kampaniyi yati iziperekanso ndalama zokwana K200,000 kwa ochemelera wapamwamba, K100,000 kwa katswiri osewera m’modzi pamwezi, komanso K500,000 kwa osewera mbambande kumathero a season ya […]

The post Dedza Dynamos yatola chi 100 million  appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください