David Mbewe wati azabweletsa ngongole zopanda chiwongola dzanja

Mtsogoleri wachipani cha Liberation for Economic Freedom (LEF) David Mbewe wati iye akazavoteledwa kukhala mtsogoleri wa dziko lino azabweletsa ngongole zopanda chiwongola dzanja makamaka kwa anthu ochita bizinezi zosiyanasiyana m’dziko muno. Mbewe amayankhula izi dzulo ku Ntaja m’boma la Machinga komwe amakhazikitsa ntchito yake yomanga mlatho wa ndalama zokwana K130 million pa mtsinje wa Mbenjere […]

The post David Mbewe wati azabweletsa ngongole zopanda chiwongola dzanja appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください