Dan Lu watokosola aMalawi ndi nyimbo yotukwana

Anthu mdziko muno makamaka mmasamba a nchezo akulavulira zakukhosi chiyamba kale pamaimbidwe, Dan Lufani kaamba ka nyimbo yake yatsopano yomwe oyimbayu wagwiritsa ntchito mawu olaura. Munyimboyi yomwe anthu akugawana mmasamba a nchezo yomwe mutu wake ndi ‘Take My Body’, oyimbayu amene amadziwika kwambiri ndi dzina loti Dan Lu, akumuuza wachikondi wake kuti ali ndi chilakolako […]

The post Dan Lu watokosola aMalawi ndi nyimbo yotukwana appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください