Apolisi ya Nkhunga m’boma la Nkhotakota, akusakasaka dalayivala wina yemwe ananyamula chamba cha nkhaninkhani mu galimoto yomwe iye amayendetsa ndipo atazindikira kuti apolisi akumutsatira anayimika galimotoyo pa malo ena mkuliyatsa liwiro la mtondo odooka. Nkhani yonse ikuti dalayivalayu amayendetsa galimoto ya mtundu wa Minibus (Town Ace) yomwe nambala yake ndi CK 10352 ndipo anthu ena […]
The post Dalayivala wina waliyatsa liwiro nkusiya galimoto ndi matumba achamba atazindikira kuti payipa appeared first on Malawi 24.