Chule anakana m’madzi muli mwake: a Matola ati a Malawi atanthauzira molakwika mwambi wawo

Pamene anthu akupitilira kukakamiza nduna yowona za mphamvu ya magetsi a Ibrahim Matola kuti apepese pazomwe anayankhula dzulo m’boma la Dedza, a Matola ati anthu sakutanthauzira bwino mwambi omwe iwo anapeleka. A Matola akudzudzulidwa kaamba konena kuti anthu omwe akudandaula kuti a Lazarus Chakwera akuyendayenda kwambiri ndi achule. Potsatira nkhaniyi, anthu oyankhula pazinthu zosiyanasiyana komaso […]

The post Chule anakana m’madzi muli mwake: a Matola ati a Malawi atanthauzira molakwika mwambi wawo appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください

コメントを残す

メールアドレスが公開されることはありません。 が付いている欄は必須項目です