Mnyamata wina wa zaka 18 ku Balaka ali mu ululu owopsa pomwe wanyenyedwa mwendo ndi sitima yomwe anaidumphira ikuyenda kuti akabemo mafuta. Malingana ndi ofalitsa nkhani pa polisi ya Balaka a Gladson M’bumpha, ovulazidwayu wazindikilidwa ngati a Lawrence Yakobe omwe akumana ndi zakudazi lachitatu pa 22 November, 2023. A M’bumpha ati Yakobe anadumphira sitima ya […]
The post Choipa chitsata mwini: sitima yanyenya mwendo wa ofuna kuba mafuta appeared first on Malawi 24.