Zadziwika kuti ophunzira ambiri a mu sukulu za ukachenjede chingerezi chikumawapeta ndipo ambiri sakwanitsa kufotokoza komanso kulemba m’chizungu chomveka bwino. Izi ndi malingana ndi otsatira kwa wachiwiri wa Chancellor ku sukulu ya ukachenjede ya University of Malawi (UNIMA), Dr Sunduzwayo Madise yemwe wati kusowa kwa ukadaulo pa kaphunzitsidwe kamakono maka kuyambira ku m’mela mpoyamba kukuwonjezera kuvutika […]
The post Chizungu chikucheka ma galajuweti amene – atero a UNIMA appeared first on Malawi 24.