Chizindikiro cha chipani chatsopano chiutsa mtsutso

Mtsutso wabuka pa masamba a nchezo pa nkhani ya chizindikiro cha chipani chomwe  changobadwa kumene cha People’s Development Party (PDP). Chipanichi, chomwe mtsogoleri wake ndi membala wakale wa chipani cha  Democratic Progressive Party (DPP), Kondwani Nankhumwa, chagwiritsa ntchito mbalame ya Nkhwazi ngati chizindikiro chake. Pomwe anthu ena sakuonapo vuto, ena akuti ma kampani ena amagwiritsa […]

The post Chizindikiro cha chipani chatsopano chiutsa mtsutso appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください