Chiyembekezo cha a Malawi chikhale mwa a Chilima  – atero a Kaliati

Patricia Kaliati yemwe ndi mlembi wamkulu wa chipani cha UTM wauza a Malawi kuti akuyenera kuyika maso komanso chiyembekezo pa a Saulos Chilima yemwe ndi mtsogoleri wachipanichi. A Kaliati amayankhula izi dzulo m’boma la Kasungu pamwambo olandira mamembala okwana 79 omwe ali adindo  komanso anthu ena osiyanasiyana ochokera mzipani monga za AFORD, MCP ndi DPP.  […]

The post Chiyembekezo cha a Malawi chikhale mwa a Chilima  – atero a Kaliati appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください