Chipatala cha Mzuzu chikuwumiliza odwala kuti azilipira thandizo la opareshoni-kafukufuku

Odwala omwe akufuna kupeza thandizo la mankhwala pa chipatala chachikulu cha Mzuzu awulura kuti ogwira ntchito ena akuwumiliza odwalawa kulipira ndalama ngati akufuna kuthandizidwa mwachangu pofuna kupangidwa opareshoni pa chipatalachi. Malingana ndi kafukufuku yemwe Malawi24 inapanga, zikuwonetsa kuti odwala ena atha miyezi yoposa inayi asanapatsidwe thandizo la mankhwala, pomwe ena akulandilandira thandizo ngati lomweri akalipira, […]

The post Chipatala cha Mzuzu chikuwumiliza odwala kuti azilipira thandizo la opareshoni-kafukufuku appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください